Salimo 95:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Bwerani, tiyeni timulambire komanso kumugwadira.Tiyeni tigwade pamaso pa Yehova amene anatipanga.+ Yesaya 44:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova, amene anakupanga+Ndiponso amene anakuumba,Amene wakhala akukuthandiza kuyambira uli mʼmimba,* wanena kuti: ‘Usachite mantha, iwe mtumiki wanga Yakobo,+Ndiponso iwe Yesuruni,*+ amene ndakusankha.
2 Yehova, amene anakupanga+Ndiponso amene anakuumba,Amene wakhala akukuthandiza kuyambira uli mʼmimba,* wanena kuti: ‘Usachite mantha, iwe mtumiki wanga Yakobo,+Ndiponso iwe Yesuruni,*+ amene ndakusankha.