-
Salimo 31:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Ndipo anthu ondidziwa amachita nane mantha.
Akandiona ndili panja amandithawa.+
-
-
Yohane 1:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Anabwera kudziko lakwawo, koma anthu akwawo enieniwo sanamulandire.
-