Salimo 51:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu Yehova, tsegulani milomo yangayi,Kuti pakamwa panga patamande inu.+ Aheberi 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu kudzera mwa Yesu.+ Kuchita zimenezi kuli ngati nsembe imene tikupereka kwa Mulungu ndipo timagwiritsa ntchito milomo yathu+ polengeza dzina lake.+
15 Tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu kudzera mwa Yesu.+ Kuchita zimenezi kuli ngati nsembe imene tikupereka kwa Mulungu ndipo timagwiritsa ntchito milomo yathu+ polengeza dzina lake.+