-
2 Samueli 12:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Choncho lupanga silidzachoka panyumba yako+ chifukwa wandinyoza potenga mkazi wa Uriya Muhiti kukhala mkazi wako.’ 11 Yehova wanena kuti, ‘Ndikugwetsera tsoka kuchokera mʼnyumba yako+ yomwe komanso iwe ukuona. Ndidzatenga akazi ako nʼkuwapereka kwa mwamuna wina,+ ndipo iye adzagona ndi akazi akowo masanasana.+
-