Salimo 50:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kumwamba kukulengeza kuti iye ndi wachilungamo,Chifukwa Mulungu ndi Woweruza.+ (Selah) Salimo 58:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako anthu adzati: “Ndithudi wolungama amalandira mphoto.+ Ndithudi pali Mulungu amene amaweruza padziko lapansi.”+
11 Kenako anthu adzati: “Ndithudi wolungama amalandira mphoto.+ Ndithudi pali Mulungu amene amaweruza padziko lapansi.”+