Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Yehova amasaukitsa ndiponso amalemeretsa,+

      Iye amatsitsa komanso amakweza.+

  • Danieli 2:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Iye amasintha nthawi ndi nyengo,+

      Amachotsa mafumu komanso kuika mafumu,+

      Amapereka nzeru kwa anthu anzeru ndiponso amachititsa kuti anthu ozindikira adziwe zinthu.+

  • Danieli 4:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Alonda ndi amene alamula zimenezi.+ Amithenga oyera ndi amene apempha zimenezi nʼcholinga chakuti anthu adziwe kuti Mulungu Wamʼmwambamwamba ndi Wolamulira wa maufumu a anthu,+ ndiponso adziwe kuti iye amapereka ulamuliro kwa aliyense amene akufuna kumupatsa ndipo amaika ngakhale munthu wonyozeka kwambiri kuti azilamulira.”

  • Luka 1:52
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 52 Watsitsa anthu amphamvu pamipando yachifumu+ ndipo wakweza anthu onyozeka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena