Salimo 74:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumbukirani anthu* amene munawatenga kalekale kuti akhale anu,+Fuko limene munaliwombola kuti likhale cholowa chanu.+ Kumbukirani phiri la Ziyoni kumene inu mumakhala.+ Salimo 132:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa Yehova wasankha Ziyoni.+Akufunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye akuti:+ Salimo 135:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova amene akukhala ku Yerusalemu,+Atamandidwe mu Ziyoni.+ Tamandani Ya!+
2 Kumbukirani anthu* amene munawatenga kalekale kuti akhale anu,+Fuko limene munaliwombola kuti likhale cholowa chanu.+ Kumbukirani phiri la Ziyoni kumene inu mumakhala.+