2 Mbiri 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Maufumu onse amʼdzikolo atamva kuti Yehova wagonjetsa adani a Isiraeli, anakhala ndi mantha ochokera kwa Mulungu.+ Salimo 2:4, 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amene wakhala pampando wachifumu kumwamba adzaseka.Yehova adzawanyogodola. 5 Pa nthawiyo, adzalankhula nawo atakwiya,Ndipo adzawachititsa mantha ndi mkwiyo wake.
29 Maufumu onse amʼdzikolo atamva kuti Yehova wagonjetsa adani a Isiraeli, anakhala ndi mantha ochokera kwa Mulungu.+
4 Amene wakhala pampando wachifumu kumwamba adzaseka.Yehova adzawanyogodola. 5 Pa nthawiyo, adzalankhula nawo atakwiya,Ndipo adzawachititsa mantha ndi mkwiyo wake.