Salimo 147:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova amakweza anthu ofatsa,+Koma anthu oipa amawagwetsera pansi. Miyambo 3:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Onyoza, iye amawanyoza,+Koma ofatsa amawakomera mtima.+ Zefaniya 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Funafunani Yehova,+ inu nonse ofatsa* apadziko lapansi,Amene mumatsatira malamulo ake olungama.* Yesetsani kukhala olungama, yesetsani kukhala ofatsa.* Mwina mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+
3 Funafunani Yehova,+ inu nonse ofatsa* apadziko lapansi,Amene mumatsatira malamulo ake olungama.* Yesetsani kukhala olungama, yesetsani kukhala ofatsa.* Mwina mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+