Salimo 42:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nʼchifukwa chiyani ndataya mtima?+ Nʼchifukwa chiyani ndikuvutika mumtima mwanga? Ndidzayembekezera Mulungu,+Ndidzamutamanda chifukwa iye ndi Mpulumutsi wanga Wamkulu.+
5 Nʼchifukwa chiyani ndataya mtima?+ Nʼchifukwa chiyani ndikuvutika mumtima mwanga? Ndidzayembekezera Mulungu,+Ndidzamutamanda chifukwa iye ndi Mpulumutsi wanga Wamkulu.+