Salimo 74:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 74 Inu Mulungu, nʼchifukwa chiyani mwatikana mpaka kalekale?+ Nʼchifukwa chiyani mkwiyo wanu ukuyakira* nkhosa zimene mukuweta?+
74 Inu Mulungu, nʼchifukwa chiyani mwatikana mpaka kalekale?+ Nʼchifukwa chiyani mkwiyo wanu ukuyakira* nkhosa zimene mukuweta?+