1 Mbiri 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muimbireni, muimbireni nyimbo* zomutamanda,+Ganizirani mozama* ntchito zake zonse zodabwitsa.+ Salimo 143:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikukumbukira masiku akale.Ndimaganizira mozama zochita zanu zonse.+Ndimaganizira* ntchito ya manja anu ndi mtima wonse.
5 Ndikukumbukira masiku akale.Ndimaganizira mozama zochita zanu zonse.+Ndimaganizira* ntchito ya manja anu ndi mtima wonse.