Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 14:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mose anatambasula dzanja lake nʼkuloza panyanja,+ ndipo Yehova anachititsa kuti mphepo yamphamvu yakumʼmawa igawe nyanjayo usiku wonse nʼkuumitsa pansi pake.+ Choncho madziwo anagawanika.+

  • Yoswa 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 madzi ochokera kumtunda anaima ngati khoma. Ndipo anakhala ngati damu lomwe linasefukira mpaka kukafika kutali kwambiri. Izi zinachitikira ku Adamu, mzinda woyandikana ndi mzinda wa Zeretani. Koma madzi akumunsi omwe ankapita kunyanja ya Araba, yomwe ndi Nyanja Yamchere,* anaphwa. Choncho, madzi a mtsinjewo anagawikana, ndipo anthuwo anawolokera kutsidya lina, pafupi ndi Yeriko.

  • Salimo 114:1-3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 114 Isiraeli atatuluka mu Iguputo,+

      Nyumba ya Yakobo itatuluka pakati pa anthu olankhula chilankhulo chachilendo,

       2 Yuda anakhala malo ake opatulika,

      Ndipo Isiraeli linakhala dziko limene ankalilamulira.+

       3 Nyanja inaona zimenezi ndipo inathawa,+

      Yorodano anabwerera mʼmbuyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena