Ekisodo 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pofuna kuwatsogolera, Yehova ankayenda patsogolo pawo. Masana ankawatsogolera pogwiritsa ntchito chipilala cha mtambo+ ndipo usiku ankawatsogolera pogwiritsa ntchito chipilala cha moto kuti chiziwaunikira. Choncho ankatha kuyenda masana komanso usiku.+ Salimo 78:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Kenako anatulutsa anthu ake mʼdzikolo ngati gulu la nkhosa,+Ndipo anawatsogolera mʼchipululu ngati nkhosa.
21 Pofuna kuwatsogolera, Yehova ankayenda patsogolo pawo. Masana ankawatsogolera pogwiritsa ntchito chipilala cha mtambo+ ndipo usiku ankawatsogolera pogwiritsa ntchito chipilala cha moto kuti chiziwaunikira. Choncho ankatha kuyenda masana komanso usiku.+
52 Kenako anatulutsa anthu ake mʼdzikolo ngati gulu la nkhosa,+Ndipo anawatsogolera mʼchipululu ngati nkhosa.