Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 1:5, 6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Munthu wanzeru amamvetsera ndipo amaphunzira zinthu zambiri.+

      Munthu womvetsa zinthu amapeza malangizo anzeru+

       6 Omuthandiza kumvetsa mwambi komanso mawu ovuta kuwamvetsa,*

      Mawu a anthu anzeru ndi mikuluwiko yawo.+

  • Mateyu 13:34, 35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Yesu analankhula zonsezi ndi gulu la anthulo pogwiritsa ntchito mafanizo. Ndithudi, nthawi zonse iye ankalankhula nawo pogwiritsa ntchito mafanizo,+ 35 kuti zimene Mulungu ananena kudzera mwa mneneri zikwaniritsidwe. Mneneriyo anati: “Ndidzatsegula pakamwa panga nʼkunena mafanizo. Ndidzafalitsa zinthu zimene zinabisika kuchokera pachiyambi.”*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena