Ekisodo 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno pa tsiku limenelo mudzauze ana anu kuti, ‘Tikuchita izi chifukwa cha zimene Yehova anatichitira potuluka mu Iguputo.’+ Salimo 44:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Inu Mulungu, ife tamva ndi makutu athu,Makolo athu anatifotokozera+Ntchito zimene inu munachita mu nthawi yawo,Mʼmasiku akale.
8 Ndiyeno pa tsiku limenelo mudzauze ana anu kuti, ‘Tikuchita izi chifukwa cha zimene Yehova anatichitira potuluka mu Iguputo.’+
44 Inu Mulungu, ife tamva ndi makutu athu,Makolo athu anatifotokozera+Ntchito zimene inu munachita mu nthawi yawo,Mʼmasiku akale.