Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 24:12, 13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Yehoyakini mfumu ya Yuda anapita kwa mfumu ya Babulo+ pamodzi ndi mayi ake, atumiki ake, akalonga ake ndi nduna za panyumba yake+ ndipo mfumu ya Babuloyo inamutenga nʼkupita naye ku ukapolo mʼchaka cha 8 cha ufumu wake.+ 13 Mfumu ya Babulo inatenga chuma chonse cha mʼnyumba ya Yehova ndi chuma cha mʼnyumba ya mfumu.+ Inaphwanyaphwanyanso ziwiya zonse zagolide zimene Solomo mfumu ya Isiraeli anapanga kuti zikhale za mʼkachisi wa Yehova.+ Zimenezi zinachitika mogwirizana ndi zimene Yehova analosera.

  • Salimo 74:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Pitani kumalo amene akhala owonongeka kuyambira kalekale.+

      Mdani wawononga chilichonse mʼmalo opatulika.+

  • Salimo 74:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Anawotcha malo anu opatulika.+

      Anaipitsa chihema chokhala ndi dzina lanu nʼkuchigwetsera pansi.

  • Maliro 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mdani wamulanda zinthu zake zonse zamtengo wapatali.+

      Yerusalemu waona anthu a mitundu ina akulowa mʼmalo ake opatulika,+

      Mitundu imene munalamula kuti isamalowe mumpingo wanu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena