Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 44:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Munathamangitsa anthu a mitundu ina ndi dzanja lanu,+

      Ndipo dziko lawo munalipereka kwa makolo athu.+

      Munagonjetsa mitundu ya anthu nʼkuithamangitsa.+

  • Salimo 78:55
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 55 Iye anathamangitsa mitundu ya anthu kuichotsa pamaso pawo.+

      Iye anawagawira dzikolo kuti likhale cholowa chawo pochita kuwayezera ndi chingwe.+

      Anachititsa mafuko a Isiraeli kuti akhale mʼnyumba zawozawo.+

  • Yeremiya 2:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ine ndinakudzala ngati mtengo wa mpesa wofiira,+ wabwino kwambiri umene unamera kuchokera ku mbewu yabwino kwambiri.

      Ndiye wandisinthira bwanji nʼkukhala mphukira zachabechabe za mtengo wa mpesa wachilendo?’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena