Yesaya 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ndikuuzaniZimene ndichite ndi munda wanga wa mpesawu: Ndichotsa zomera zimene zinali ngati mpanda wa mundawo,Ndipo uwotchedwa.+ Ndigumula mpanda wake wamiyalaNdipo mundawo udzapondedwapondedwa.
5 Tsopano ndikuuzaniZimene ndichite ndi munda wanga wa mpesawu: Ndichotsa zomera zimene zinali ngati mpanda wa mundawo,Ndipo uwotchedwa.+ Ndigumula mpanda wake wamiyalaNdipo mundawo udzapondedwapondedwa.