2 Mbiri 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno anauza oweruzawo kuti: “Muzichita zinthu mosamala chifukwa simukuweruzira munthu koma Yehova, ndipo iye ali nanu pa ntchito yoweruzayi.+
6 Ndiyeno anauza oweruzawo kuti: “Muzichita zinthu mosamala chifukwa simukuweruzira munthu koma Yehova, ndipo iye ali nanu pa ntchito yoweruzayi.+