Yohane 10:34, 35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yesu anawafunsa kuti: “Kodi mʼChilamulo chanu sanalembemo kuti, ‘Ine ndanena kuti: “Inu ndinu milungu”’?*+ 35 Ngati anthu amene anatsutsidwa ndi mawu a Mulungu omwe satha mphamvu, anawatchula kuti ‘milungu,’+ 1 Akorinto 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu amati pali milungu yambiri, kaya kumwamba kapena padziko lapansi.+ Choncho kwa anthu amenewo palidi milungu yambiri ndi ambuye ambiri.
34 Yesu anawafunsa kuti: “Kodi mʼChilamulo chanu sanalembemo kuti, ‘Ine ndanena kuti: “Inu ndinu milungu”’?*+ 35 Ngati anthu amene anatsutsidwa ndi mawu a Mulungu omwe satha mphamvu, anawatchula kuti ‘milungu,’+
5 Anthu amati pali milungu yambiri, kaya kumwamba kapena padziko lapansi.+ Choncho kwa anthu amenewo palidi milungu yambiri ndi ambuye ambiri.