Salimo 146:3, 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musamakhulupirire anthu olemekezeka*Kapena mwana wa munthu amene sangabweretse chipulumutso.+ 4 Mpweya* wake umachoka, ndipo iye amabwerera kunthaka.+Pa tsiku limenelo zonse zimene amaganiza zimatheratu.+
3 Musamakhulupirire anthu olemekezeka*Kapena mwana wa munthu amene sangabweretse chipulumutso.+ 4 Mpweya* wake umachoka, ndipo iye amabwerera kunthaka.+Pa tsiku limenelo zonse zimene amaganiza zimatheratu.+