-
Salimo 92:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Koma inu Yehova, ndinu wokwezeka mpaka kalekale.
-
-
Danieli 4:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Alonda ndi amene alamula zimenezi.+ Amithenga oyera ndi amene apempha zimenezi nʼcholinga chakuti anthu adziwe kuti Mulungu Wamʼmwambamwamba ndi Wolamulira wa maufumu a anthu,+ ndiponso adziwe kuti iye amapereka ulamuliro kwa aliyense amene akufuna kumupatsa ndipo amaika ngakhale munthu wonyozeka kwambiri kuti azilamulira.”
-