Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 27:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ndapempha chinthu chimodzi kwa Yehova,

      Chimenecho ndi chimene ndikuchilakalaka.

      Chinthu chake nʼchakuti, ndikhale mʼnyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga,+

      Kuti ndione ubwino wa Yehova,

      Komanso kuti ndiyangʼane kachisi wake* moyamikira.*+

  • Salimo 43:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Tumizani kuwala kwanu ndi choonadi chanu.+

      Zimenezi zinditsogolere.+

      Zinditsogolere kuphiri lanu lopatulika ndi kuchihema chanu chachikulu.+

  • Salimo 46:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Pali mtsinje umene nthambi zake zimachititsa kuti anthu amumzinda wa Mulungu asangalale,+

      Chihema chachikulu chopatulika cha Wamʼmwambamwamba.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena