Salimo 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndithu, masiku onse a moyo wanga ndidzasangalala ndi ubwino wanu komanso chikondi chanu chokhulupirika,+Ndipo ndidzakhala mʼnyumba ya Yehova kwa moyo wanga wonse.+ Salimo 65:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wosangalala ndi munthu amene inu mwamusankha nʼkumubweretsa pafupi ndi inu,Kuti akhale mʼmabwalo anu.+ Tidzakhutira ndi zinthu zabwino zamʼnyumba yanu,+Kachisi wanu woyera.*+
6 Ndithu, masiku onse a moyo wanga ndidzasangalala ndi ubwino wanu komanso chikondi chanu chokhulupirika,+Ndipo ndidzakhala mʼnyumba ya Yehova kwa moyo wanga wonse.+
4 Wosangalala ndi munthu amene inu mwamusankha nʼkumubweretsa pafupi ndi inu,Kuti akhale mʼmabwalo anu.+ Tidzakhutira ndi zinthu zabwino zamʼnyumba yanu,+Kachisi wanu woyera.*+