Salimo 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova, ndimakonda nyumba imene inu mumakhala,+Malo amene kumakhala ulemerero wanu.+ Salimo 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndapempha chinthu chimodzi kwa Yehova,Chimenecho ndi chimene ndikuchilakalaka.Chinthu chake nʼchakuti, ndikhale mʼnyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga,+Kuti ndione ubwino wa Yehova,Komanso kuti ndiyangʼane kachisi wake* moyamikira.*+ Salimo 43:3, 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tumizani kuwala kwanu ndi choonadi chanu.+ Zimenezi zinditsogolere.+Zinditsogolere kuphiri lanu lopatulika ndi kuchihema chanu chachikulu.+ 4 Kenako ndidzapita paguwa lansembe la Mulungu,+Kwa Mulungu amene amandisangalatsa kwambiri. Ndipo ndidzakutamandani ndi zeze+ inu Mulungu, Mulungu wanga.
4 Ndapempha chinthu chimodzi kwa Yehova,Chimenecho ndi chimene ndikuchilakalaka.Chinthu chake nʼchakuti, ndikhale mʼnyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga,+Kuti ndione ubwino wa Yehova,Komanso kuti ndiyangʼane kachisi wake* moyamikira.*+
3 Tumizani kuwala kwanu ndi choonadi chanu.+ Zimenezi zinditsogolere.+Zinditsogolere kuphiri lanu lopatulika ndi kuchihema chanu chachikulu.+ 4 Kenako ndidzapita paguwa lansembe la Mulungu,+Kwa Mulungu amene amandisangalatsa kwambiri. Ndipo ndidzakutamandani ndi zeze+ inu Mulungu, Mulungu wanga.