Levitiko 26:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Choncho ndidzakumbukira pangano limene ndinachita ndi Yakobo,+ Isaki+ komanso Abulahamu.+ Ndidzakumbukiranso dzikolo. Yoweli 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Yehova adzachitira nsanje dziko lake,Ndipo adzachitira chifundo anthu ake.+
42 Choncho ndidzakumbukira pangano limene ndinachita ndi Yakobo,+ Isaki+ komanso Abulahamu.+ Ndidzakumbukiranso dzikolo.