Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Awa ndi anthu amʼchigawo* amene anatuluka mu ukapolo+ pa anthu omwe Nebukadinezara mfumu ya ku Babulo anawatengera ku Babulo.+ Anthuwa anabwerera ku Yerusalemu ndi ku Yuda, aliyense kumzinda wakwawo.+

  • Yeremiya 30:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Yehova wanena kuti:

      “Ndikusonkhanitsa anthu amʼmatenti a Yakobo amene anagwidwa nʼkutengedwa kupita kudziko lina,+

      Ndipo ndidzamvera chisoni malo okhala a Yakobo.

      Mzinda udzamangidwanso pamalo amene unali poyamba,+

      Ndipo nsanja yokhala ndi mpanda wolimba idzakhala pamalo ake oyenerera.

  • Ezekieli 39:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ndidzabwezeretsa ana a Yakobo+ omwe anatengedwa kupita kumayiko ena ndipo ndidzachitira chifundo nyumba yonse ya Isiraeli.+ Ndi mphamvu zanga zonse, ndidzateteza dzina langa loyera.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena