Salimo 103:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye sadzakhalira kutipezera zifukwa nthawi zonse,+Kapena kutisungira mkwiyo mpaka kalekale.+ Yesaya 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa tsiku limenelo ndithu udzanena kuti: “Ndikukuthokozani, inu YehovaChifukwa ngakhale munandikwiyira,Mkwiyo wanu unachepa pangʼonopangʼono ndipo munanditonthoza.+
12 Pa tsiku limenelo ndithu udzanena kuti: “Ndikukuthokozani, inu YehovaChifukwa ngakhale munandikwiyira,Mkwiyo wanu unachepa pangʼonopangʼono ndipo munanditonthoza.+