-
Deuteronomo 8:17, 18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ngati mumtima mwanu munganene kuti, ‘Chuma ichi ndachipeza chifukwa cha ntchito ya manja anga komanso mphamvu zanga,’+ 18 muzikumbukira kuti ndi Yehova Mulungu wanu amene amakupatsani mphamvu kuti mupeze chuma,+ pofuna kusunga pangano lake limene analumbira kwa makolo anu, ngati mmene zilili lero.+
-
-
Salimo 78:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Zikadzatero anawo azidzadalira Mulungu.
-