Yesaya 46:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ine ndabweretsa pafupi chilungamo changa.Chilungamocho sichili kutali,Ndipo chipulumutso changa sichidzachedwa.+ Ndidzapereka chipulumutso mu Ziyoni, ndipo Isiraeli ndidzamʼpatsa ulemerero wanga.”+
13 Ine ndabweretsa pafupi chilungamo changa.Chilungamocho sichili kutali,Ndipo chipulumutso changa sichidzachedwa.+ Ndidzapereka chipulumutso mu Ziyoni, ndipo Isiraeli ndidzamʼpatsa ulemerero wanga.”+