Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 26:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Usiku ndimakulakalakani ndi mtima wanga wonse,

      Inde, ndimakufunafunani ndi mtima wonse.+

      Chifukwa mukaweruza dziko lapansi,

      Anthu okhala mʼdzikoli amaphunzira zokhudza chilungamo.+

  • Yesaya 45:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Inu kumwamba, chititsani kuti mvula igwe.+

      Chititsani kuti mitambo igwetse chilungamo ngati mvula.

      Dziko lapansi litseguke ndipo libale chipulumutso,

      Pa nthawi imodzimodziyo lichititse kuti chilungamo chiphuke.+

      Ine Yehova ndachititsa zimenezi.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena