Chivumbulutso 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Popeza inu nokha Yehova* ndinu wokhulupirika, ndi ndani amene sadzakuopani komanso kulemekeza dzina lanu?+ Anthu a mitundu yonse adzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa iwo adziwa malamulo anu olungama.”
4 Popeza inu nokha Yehova* ndinu wokhulupirika, ndi ndani amene sadzakuopani komanso kulemekeza dzina lanu?+ Anthu a mitundu yonse adzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa iwo adziwa malamulo anu olungama.”