Yobu 33:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iye wandiwombola* kuti ndisapite kudzenje,*+Ndipo moyo wanga udzaona kuwala.’ Salimo 56:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa inu mwandipulumutsa* ku imfa.+Ndipo mwateteza phazi langa kuti lisapunthwe,+Kuti ndiyende pamaso pa Mulungu mʼkuwala kumene kumaunikira anthu amoyo.+ Salimo 116:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu mwandipulumutsa ku imfa,Mwapukuta misozi yanga ndipo mwateteza phazi langa kuti lisapunthwe.+
13 Chifukwa inu mwandipulumutsa* ku imfa.+Ndipo mwateteza phazi langa kuti lisapunthwe,+Kuti ndiyende pamaso pa Mulungu mʼkuwala kumene kumaunikira anthu amoyo.+