Salimo 78:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Koma anasankha fuko la Yuda,+Phiri la Ziyoni limene amalikonda.+ Salimo 132:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa Yehova wasankha Ziyoni.+Akufunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye akuti:+