Salimo 48:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Phiri la Ziyoni limene lili mʼdera lakutali lakumpoto,Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka komanso anthu padziko lonse lapansi akusangalala nalo,+Ndipo ndi mzinda wa Mfumu Yaikulu.+ Yesaya 60:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ana a anthu amene ankakupondereza adzabwera nʼkudzagwada pamaso pako.Anthu onse amene ankakuchitira zachipongwe adzagwada pamapazi ako,Ndipo adzakutchula kuti mzinda wa Yehova,Ziyoni wa Woyera wa Isiraeli.+
2 Phiri la Ziyoni limene lili mʼdera lakutali lakumpoto,Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka komanso anthu padziko lonse lapansi akusangalala nalo,+Ndipo ndi mzinda wa Mfumu Yaikulu.+
14 Ana a anthu amene ankakupondereza adzabwera nʼkudzagwada pamaso pako.Anthu onse amene ankakuchitira zachipongwe adzagwada pamapazi ako,Ndipo adzakutchula kuti mzinda wa Yehova,Ziyoni wa Woyera wa Isiraeli.+