Salimo 89:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwaphwanya Rahabi*+ ngati munthu amene waphedwa.+ Mwabalalitsa adani anu ndi dzanja lanu lamphamvu.+ Yesaya 30:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa thandizo lochokera ku Iguputo ndi losathandiza ngakhale pangʼono.+ Choncho iye ndamutchula kuti: “Rahabi+ amene amangokhala osachita chilichonse.”
10 Mwaphwanya Rahabi*+ ngati munthu amene waphedwa.+ Mwabalalitsa adani anu ndi dzanja lanu lamphamvu.+
7 Chifukwa thandizo lochokera ku Iguputo ndi losathandiza ngakhale pangʼono.+ Choncho iye ndamutchula kuti: “Rahabi+ amene amangokhala osachita chilichonse.”