Salimo 141:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 141 Inu Yehova, ine ndakuitanani.+ Bwerani mofulumira kuti mudzandithandize.+ Mutchere khutu ndikamakuitanani.+
141 Inu Yehova, ine ndakuitanani.+ Bwerani mofulumira kuti mudzandithandize.+ Mutchere khutu ndikamakuitanani.+