Yobu 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa cha kuzunzika, maso anga ayamba kuchita mdima.+Manja ndi miyendo yanga zakhala ngati mthunzi. Salimo 42:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Misozi yanga ili ngati chakudya changa masana ndi usiku.Anthu amandinyoza tsiku lonse kuti: “Mulungu wako ali kuti?”+ Maliro 3:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Maso anga akungotuluka misozi ndipo sikusiya,+
7 Chifukwa cha kuzunzika, maso anga ayamba kuchita mdima.+Manja ndi miyendo yanga zakhala ngati mthunzi.
3 Misozi yanga ili ngati chakudya changa masana ndi usiku.Anthu amandinyoza tsiku lonse kuti: “Mulungu wako ali kuti?”+