Salimo 55:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Usiku, mʼmawa ndi masana ndimavutika ndipo ndimabuula,*+Koma Mulungu amamva mawu anga.+