Yobu 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Nʼchifukwa chiyani mukubisa nkhope yanu,+Nʼkumandiona ngati mdani wanu?+ Salimo 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi mudzandiiwala mpaka liti, inu Yehova? Mpaka kalekale? Kodi mudzandibisira nkhope yanu mpaka liti?+
13 Kodi mudzandiiwala mpaka liti, inu Yehova? Mpaka kalekale? Kodi mudzandibisira nkhope yanu mpaka liti?+