-
Salimo 31:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Ndipo anthu ondidziwa amachita nane mantha.
Akandiona ndili panja amandithawa.+
-
-
Salimo 38:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Anzanga komanso anthu amene ndimawakonda akundisala chifukwa cha mliri wanga,
Ndipo anthu oyandikana nawo sakufuna kukhala nane pafupi.
-
-
Salimo 142:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Palibenso kulikonse kumene ndingathawire,+
Ndipo palibe amene akundidera nkhawa.
-