1 Samueli 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Palibe woyera ngati Yehova,Palibenso wina koma inu nokha,+Ndipo palibe thanthwe lofanana ndi Mulungu wathu.+ Salimo 84:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,Wosangalala ndi munthu amene amakukhulupirirani.+
2 Palibe woyera ngati Yehova,Palibenso wina koma inu nokha,+Ndipo palibe thanthwe lofanana ndi Mulungu wathu.+