Salimo 80:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dzanja lanu lithandize munthu amene ali kudzanja lanu lamanja,Lithandize mwana wa munthu amene mwamupatsa mphamvu kuti mulemekezeke.+ Yesaya 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndikumuthandiza, Wosankhidwa wanga+ amene amandisangalatsa,+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye.+Iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+
17 Dzanja lanu lithandize munthu amene ali kudzanja lanu lamanja,Lithandize mwana wa munthu amene mwamupatsa mphamvu kuti mulemekezeke.+
42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndikumuthandiza, Wosankhidwa wanga+ amene amandisangalatsa,+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye.+Iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+