2 Samueli 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nkhondo ya pakati pa anthu a nyumba ya Sauli ndi a nyumba ya Davide inapitirirabe. Davide anapitiriza kukhala wamphamvu+ koma anthu a nyumba ya Sauli ankachepa mphamvu.+ 2 Samueli 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ine ndidzakhala nawe kulikonse kumene ungapite,+ ndipo ndidzagonjetsa adani ako onse pamaso pako.+ Ndidzachititsa kuti dzina lako lidziwike+ ngati mmene zimakhalira ndi anthu otchuka mʼdzikoli.
3 Nkhondo ya pakati pa anthu a nyumba ya Sauli ndi a nyumba ya Davide inapitirirabe. Davide anapitiriza kukhala wamphamvu+ koma anthu a nyumba ya Sauli ankachepa mphamvu.+
9 Ine ndidzakhala nawe kulikonse kumene ungapite,+ ndipo ndidzagonjetsa adani ako onse pamaso pako.+ Ndidzachititsa kuti dzina lako lidziwike+ ngati mmene zimakhalira ndi anthu otchuka mʼdzikoli.