1 Mafumu 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Solomo ankalamulira maufumu onse kuyambira ku Mtsinje*+ mpaka kudziko la Afilisiti nʼkukafika kumalire ndi Iguputo. Maufumuwa ankabweretsa msonkho kwa Solomo komanso kumutumikira kwa moyo wake wonse.+ Salimo 72:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye adzakhala ndi anthu omugonjera* kuchokera kunyanja kukafika kunyanja,Komanso kuchokera ku Mtsinje* kukafika kumalekezero a dziko lapansi.+
21 Solomo ankalamulira maufumu onse kuyambira ku Mtsinje*+ mpaka kudziko la Afilisiti nʼkukafika kumalire ndi Iguputo. Maufumuwa ankabweretsa msonkho kwa Solomo komanso kumutumikira kwa moyo wake wonse.+
8 Iye adzakhala ndi anthu omugonjera* kuchokera kunyanja kukafika kunyanja,Komanso kuchokera ku Mtsinje* kukafika kumalekezero a dziko lapansi.+