2 Samueli 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ine ndidzakhala bambo ake ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Akalakwitsa zinthu zina, ine ndidzamudzudzula ndi ndodo ya anthu ndi zikoti za ana a anthu.*+ 1 Mafumu 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Yehova anabweretsa munthu woti azilimbana ndi Solomo.+ Munthuyo anali Hadadi wa ku Edomu ndipo anali wa mʼbanja lachifumu ku Edomuko.+ 1 Mafumu 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Atatero, anauza Yerobowamu kuti: “Tengapo mapisi 10, chifukwa Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndikungʼamba ufumuwu kuuchotsa mʼmanja mwa Solomo ndipo iwe ndidzakupatsa mafuko 10.+
14 Ine ndidzakhala bambo ake ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Akalakwitsa zinthu zina, ine ndidzamudzudzula ndi ndodo ya anthu ndi zikoti za ana a anthu.*+
14 Kenako Yehova anabweretsa munthu woti azilimbana ndi Solomo.+ Munthuyo anali Hadadi wa ku Edomu ndipo anali wa mʼbanja lachifumu ku Edomuko.+
31 Atatero, anauza Yerobowamu kuti: “Tengapo mapisi 10, chifukwa Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndikungʼamba ufumuwu kuuchotsa mʼmanja mwa Solomo ndipo iwe ndidzakupatsa mafuko 10.+