Salimo 41:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atamandike Yehova Mulungu wa Isiraeli,Kuyambira panopo mpaka kalekale.*+ Ame! Ame! Salimo 72:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Atamandike Yehova Mulungu, Mulungu wa Isiraeli,+Iye yekha amene amachita zinthu zodabwitsa.+