Luka 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Taonani! Inetu ndakupatsani ulamuliro kuti muzitha kupondaponda njoka ndi zinkhanira. Komanso ndakupatsani ulamuliro kuti mugonjetse mphamvu zonse za mdani,+ ndipo palibe chimene chidzakuvulazeni.
19 Taonani! Inetu ndakupatsani ulamuliro kuti muzitha kupondaponda njoka ndi zinkhanira. Komanso ndakupatsani ulamuliro kuti mugonjetse mphamvu zonse za mdani,+ ndipo palibe chimene chidzakuvulazeni.