Aroma 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa “aliyense woitana pa dzina la Yehova* adzapulumuka.”+ Aheberi 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamene Khristu anali padzikoli,* anapereka mapemphero ochonderera ndiponso opempha, kwa amene akanatha kumupulumutsa ku imfa. Anapereka mapempherowa mofuula komanso akugwetsa misozi,+ ndipo anamumvera chifukwa ankaopa Mulungu.
7 Pamene Khristu anali padzikoli,* anapereka mapemphero ochonderera ndiponso opempha, kwa amene akanatha kumupulumutsa ku imfa. Anapereka mapempherowa mofuula komanso akugwetsa misozi,+ ndipo anamumvera chifukwa ankaopa Mulungu.